1 Samueli 23:2 BL92

2 Cifukwa cace Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndimuke kodi kukakantha Afilisti aja? Ndipo Yehova anati kwa Davide, Muka, nukanthe Afilisti, ndi kupulumutsa Keila.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:2 nkhani