1 Samueli 23:3 BL92

3 Ndipo anyamata a Davide ananena naye, Taonani, ife tikhalira m'mantha ku Yuda kuno; koposa kotani nanga tikafika ku Keila kuponyana ndi makamu a nkhondo a Afilisti.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:3 nkhani