1 Samueli 23:24 BL92

24 Ndipo iwo ananyamuka, namuka ku Zifi asanapiteko Sauli; koma Davide ndi anthu ace anali ku cipululu ca Maoni, m'cigwa ca kumwera kwa cipululu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:24 nkhani