1 Samueli 23:25 BL92

25 Ndipo Sauli ndi anthu ace anamuka kukamfuna. Koma wina anauza Davide; cifukwa cace anatsikira kuthanthweko, nakhala m'cipululu ca Maoni. Ndipo pamene Sauli anamva ici, iye anamlondola Davide m'cipululu ca Maoni.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:25 nkhani