1 Samueli 24:16 BL92

16 Ndipo kunali, pakutsiriza Davide kulankhula mau awa kwa Sauli, Sauli anati, Ndiwo mau ako kodi, mwana wanga Davide? Sauli nakweza mau ace, nalira misozi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:16 nkhani