15 Cifukwa cace Yehova akhale woweruza, naweruze pakati pa ine ndi inu, nayang'anire, oandigwirire moyo, oandipulumutse m'dzanja lanu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24
Onani 1 Samueli 24:15 nkhani