6 Nati kwa anyamata ace, Mulungu andiletse kucitira ici mbuye wanga, wodzozedwa wa Yehova, kumsamulira dzanja langa, popeza iye ndiye wodzozedwa wa Yehova.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24
Onani 1 Samueli 24:6 nkhani