1 Samueli 25:12 BL92

12 Comweco anyamata a Davide anatembenukira ku njira yao, nabwerera, nadza namuuza monga mwa mau onse awa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:12 nkhani