1 Samueli 25:3 BL92

3 Tsono dzina la munthuyo ndiye Nabala, ndi dzina la mkazi wace ndiye Abigayeli; ndiye mkazi wa nzeru yabwino, ndi wa nkhope yokongola; koma mwamunayo anali waphunzo ndi woipa macitidwe ace; ndipo iye anali wa banja la Kalebi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:3 nkhani