1 Samueli 25:2 BL92

2 Ndipo panali munthu ku Maoni, amene katundu wace anali ku Karimeli; iyeyu anali womveka ndithu, anali nazo nkhosa zikwi zitatu, ndi mbuzi cikwi cimodzi; ndipo analikusenga nkhosa zace ku Karimeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:2 nkhani