1 Ndipo Samueli anamwalira; ndi Aisrayeli onse anaunjikana pamodzi nalira maliro ace, namuika m'nyumba yace ku Rama. Davide nanyamuka, natsikira ku cipululu ca Parana.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25
Onani 1 Samueli 25:1 nkhani