33 ndipo, kudalitsike kucenjera kwako, nudalitsike iwe, pakuti unandiletsa kusakhetsa mwazi, ndi kusabwezera cilango ndi dzanja la ine ndekha.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25
Onani 1 Samueli 25:33 nkhani