1 Samueli 25:7 BL92

7 Ndipo tsono ndamva kuti muli nao osenga nkhosa; abusa anu amene anali ndi ife, sitinawacititsa manyazi, ndipo panalibe kanthu kao kadasowa, nthawi yonse anakhala iwo ku Karimeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:7 nkhani