1 Samueli 25:8 BL92

8 Mufunse anyamata anu, adzakuuzani; cifukwa cace muwakomere mtima anyamata awa, pakuti tirikufika tsiku labwino; mupatse ciri conse muli naco m'dzanja lanu, kwa anyamata anu, ndi kwa mwana wanu Davide.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:8 nkhani