1 Samueli 26:11 BL92

11 Yehova andiletse ine kusamula dzanja langa pa wodzozedwa wa Yehova; koma utenge mkondowo uli kumutu kwace, ndi cikho ca madzi, ndipo tiyeni, timuke.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:11 nkhani