1 Samueli 26:16 BL92

16 Ici unacicita siciri cabwino. Pali Yehova, muyenera kufa inu, cifukwa simunadikira mbuye wanu, wodzozedwa wa Yehova. Ndipo tsono, penyani mkondo wa mfumu ndi cikho ca madzi zinali kumutu kwace ziri kuti?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:16 nkhani