25 Pomwepo Sauli anati kwa Davide, Udalitsike iwe, mwana wanga Davide; udzacita ndithu camphamvu, nudzapambana. Comweco Davide anamuka, ndipo Sauli anabwera kwao.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26
Onani 1 Samueli 26:25 nkhani