1 Samueli 27:1 BL92

1 Ndipo Davide ananena mumtima mwace, Tsiku tina Sauli adzandipha; palibe cina condikomera koma kuti ndithawire ku dziko la Afilisti; ndipo Sauli adzakhala kakasi cifukwa ca ine, osandifunanso m'malire onse a Israyeli, momwemo ndidzapulumuka m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27

Onani 1 Samueli 27:1 nkhani