2 Ndipo Davide ananyamuka, naoloka pamodzi ndi anthu mazana asanu ndi limodzi amene anali naye, nafika kwa Akisi mwana wa Maoki, mfumu ya ku Gati.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27
Onani 1 Samueli 27:2 nkhani