1 Samueli 27:3 BL92

3 Ndipo Davide anakhala ndi Akisi ku Gati, iye ndi anthu ace, munthu yense ndi a pabanja pace, inde Davide ndi akazi ace awiri, Ahinoamu wa ku Jezreeli, ndi Abigayeli wa ku Karimeli, mkazi wa Nabala.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27

Onani 1 Samueli 27:3 nkhani