1 Samueli 26:5 BL92

5 Ndipo Davide ananyamuka nafika pamalo pala Sauli anamangapo; ndipo Davide adaona pogona Sauli, ndi Abineri mwana wa Neri kazembe wa khamu lace; ndipo Sauli anagona pakati pa linga la magareta, ndipo anthu adamanga zithando pomzinga pace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:5 nkhani