9 Koma Davide ananena ndi Abisai, Usamuononge, ndani adzasamula dzanja lace pa wodzozedwa wa Mulungu, ndi kukhala wosacimwa?
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26
Onani 1 Samueli 26:9 nkhani