8 Ndipo Abisai anati kwa Davide, Lero Mulungu wapereka mdani wanu m'dzanja lanu; ndiloleni ndimpyoze ndi mkondo, kamodzi kokha, sindidzampyoza kawiri.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26
Onani 1 Samueli 26:8 nkhani