1 Samueli 26:7 BL92

7 Comweco Davide ndi Abisai anafika kwa anthuwo usiku; ndipo onani, Sauli anagona tulo m'kati mwa linga la magareta, ndi mkondo wace wozika kumutu kwace; ndi Abineri ndi anthuwo anagona pomzinga iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:7 nkhani