12 Ndipo Akisi anakhulupirira Davide, nati Anadziipitsa ndithu pakati pa anthu a Israyeli, cifukwa cace iye adzakhala mnyamata wanga cikhalire.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27
Onani 1 Samueli 27:12 nkhani