1 Samueli 27:11 BL92

11 Ndipo Davide sadasunga wamoyo mwamuna kapena mkazi, kubwera nao ku Gati; popeza adati, Kuti angatiulule, ndi kuti, Davide anatero, ndi makhalidwe ace ndi otere, masiku onse akukhala ku dziko la Afilisti.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27

Onani 1 Samueli 27:11 nkhani