1 Samueli 27:10 BL92

10 Ndipo Akisi anati, Wapooyana nkhondo ndi yani lero? Nati Davide, Ndi a kumwera kwa Ayuda, ndi a kumwera kwa Ayerameli, ndi a kumwera kwa Akeni.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27

Onani 1 Samueli 27:10 nkhani