9 Ndipo Davide anapasula dzikolo, sanasunga ndi moyo mwamuna kapena wamkazi; natenga nkhosa, ndi ng'ombe, ndi aburu, ndi ngamila, ndi zobvala; nabwera nafika kwa Akisi.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27
Onani 1 Samueli 27:9 nkhani