1 Samueli 28:12 BL92

12 Ndipo mkaziyo pakuona Samueli, anapfuula ndi mau akuru; ndi mkaziyo analankhula ndi Sauli, nati, Munandinyengeranji? popeza inu ndinu Sauli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:12 nkhani