1 Samueli 28:13 BL92

13 Ndipo mfumuvo inanena naye, Usaope, kodi ulikuona ciani? Mkaziyo nanena ndi Sauli, Ndirikuona milungu irikukwera kuturuka m'kati mwa dziko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:13 nkhani