1 Samueli 28:14 BL92

14 Ndipo ananena naye, Makhalidwe ace ndi otani? nati iye, Nkhalamba irikukwera yobvala mwinjiro. Pamenepo Sauli anazindikira kuti ndi Samueli, naweramitsa nkhope yace pansi, namgwadira.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:14 nkhani