1 Samueli 28:2 BL92

2 Ndipo Davide anati kwa Akisi, Potero mudzadziwe cimene mnyamata wanu adzacita. Ndipo Akisi anati kwa Davide, Cifukwa cace ndidzakuika iwe ukhale wondisungira moyo wanga masiku onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:2 nkhani