1 Samueli 28:3 BL92

3 M'menemo Samueli ndipo atafa, ndipo Aisrayeli onse atalira maliro ace, namuika m'Rama, m'mudzi mwao. Ndipo Sauli anacotsa m'dzikomo obwebweta onse, ndi aula onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:3 nkhani