1 Samueli 28:20 BL92

20 Pomwepo Sauli anagwa pansi tantha, naopa kwakukuru, cifukwa ca mau a Samueli; ndipo analibe mphamvu; pakuti tsiku lonse ndi usiku wace wonse anakhala osadya kanthu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:20 nkhani