1 Samueli 28:21 BL92

21 Ndipo mkaziyo anafika kwa Sauli, naona kuti ali wobvutika kwambiri, nanena naye, Onani, mdzakazi wanu anamvera mau anu, ndipo ndinataya moyo wanga, ndi kumvera mau anu munalankhula ndi ine.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:21 nkhani