1 Samueli 28:7 BL92

7 Tsono Sauli anati kwa anyamata ace, Mundifunire mkazi wobwebweta, kuti ndimuke kwa iye ndi kumfunsira. Ndipo anyamata ace anati kwa iye, Onani ku Endori kuli mkazi wobwebweta.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:7 nkhani