1 Samueli 28:8 BL92

8 Ndipo Sauli anadzizimbaitsa nabvala zobvala zina, nanka iye pamodzi ndi anthu ena awiri, nafika kwa mkaziyo usiku; nati iye, Undilotere ndi mzimu wobwebwetawo, nundiukitsire ali yense ndidzakuchulira dzina lace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:8 nkhani