1 Samueli 29:1 BL92

1 Tsono Afilisti anasonkhanitsa makamu ao onse ku Afeki; ndipo Aisrayeli anamanga ku citsime ca m'Jezreeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29

Onani 1 Samueli 29:1 nkhani