2 Ndipo akalonga a Afilisti ananyamuka ndi mazana ao ndi zikwi zao; ndipo Davide ndi anthu ace ananyamuka ndi a pambuyo pamodzi ndi Akisi.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29
Onani 1 Samueli 29:2 nkhani