1 Samueli 29:8 BL92

8 Ndipo Davide ananena ndi Akisi, Koma ndinacitanji? Ndipo munapeza ciani mu mnyamata wanu nthawi yonse ndiri pamaso panu kufikira lero, kuti sindingapite kukaponyana nkhondo ndi adani a mbuye wanga mfumu?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29

Onani 1 Samueli 29:8 nkhani