1 Samueli 29:9 BL92

9 Ndipo Akisi anayankha nanena ndi Davide, Ndidziwa kuti pamaso panga uli wabwino, ngati mthenga wa Mulungu; koma akalonga a Afilisti anena, iye asamuke nafe kunkhondoko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29

Onani 1 Samueli 29:9 nkhani