1 Samueli 3:10 BL92

10 Ndipo Yehova anabwera, naimapo, namuitana monga momwemo, Samueli, Samueli. Pompo Samueli anayankha, Nenani, popeza mnyamata wanu akumva.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:10 nkhani