1 Samueli 3:9 BL92

9 Cifukwa cace Eli anati kwa Samueli, Pita, ukagone; ndipo akakuitananso, ukabvomere, kuti, Nenani, Yehova, popeza mnyamata wanu akumva. Comweco Samueli anakagona m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:9 nkhani