1 Samueli 3:8 BL92

8 Ndipo Yehova anabwereza kumuitana Samueli nthawi yacitatu. Ndipo iye anauka napita kwa Eli, nati, Ndine, pakuti mwandiitana ndithu. Ndipo Eli anazindikira kuti ndiye Yehova amene analikuitana mwanayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:8 nkhani