1 Samueli 3:5 BL92

5 Ndipo anathamangira kwa Eli nati, Ndine, popeza mwandiitana ine. Ndipo iye anati, Sindinaitana, kagone. Napita iye, nagona,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:5 nkhani