1 Samueli 3:6 BL92

6 Ndipo Yehova anabwereza kumuitana, ndi kuti, Samueli. Ndipo Samueli anauka, napita kwa Eli, nati, Ndine, pakuti mwandiitana ndithu. Koma iye anayankha, Sindinaitana, mwana wanga; kagone.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:6 nkhani