10 Ndipo Davide anawalondola, iye ndi anthu mazana anai; koma anthu mazana awiri anatsala m'mbuyo, cifukwa analema, osakhoza kuoloka kamtsinje Besori.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30
Onani 1 Samueli 30:10 nkhani