1 Samueli 30:21 BL92

21 Ndipo Davide anafika kuli anthu mazana awiri amene analema osakhoza kutsata Davide, amenenso anawakhalitsa kukamtsinje Besori; ndipo iwowa anaturuka kucingamira Davide, ndi amene anali naye; ndipo pakuyandikira Davide anawafunsa ngati ali bwanji.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:21 nkhani