1 Samueli 30:22 BL92

22 Pamenepo anthu oipa onse, ndi opanda pace a iwo amene anapita ndi Davide anayankha nati, Popeza sadamuka nafe sitidzawapatsa kanthu ka zofunkha tidazilanditsa, koma kwa munthu yense mkazi wace ndi ana ace, kuti acoke nao namuke.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:22 nkhani