24 Ndipo ndani adzabvomerezana nanu mrandu uwu? Pakuti monga gawo lace la iye wakumuka kunkhondoko, momwemo lidzakhala gawo lace la iye wakukhala ndi akatundu, adzagawana cimodzimodzi.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30
Onani 1 Samueli 30:24 nkhani